2 Mbiri 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anaiuza kuti: “Mukakhala munthu wabwino kwa anthuwa ndi kuchita zowasangalatsa, ndiponso mukawayankha ndi mawu abwino,+ iwo adzakhala atumiki anu nthawi zonse.”+
7 Iwo anaiuza kuti: “Mukakhala munthu wabwino kwa anthuwa ndi kuchita zowasangalatsa, ndiponso mukawayankha ndi mawu abwino,+ iwo adzakhala atumiki anu nthawi zonse.”+