2 Mbiri 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Asa anamukwiyira wamasomphenyayo. Kenako anamuika m’ndende n’kumumanga m’matangadza+ popeza anamupsera mtima kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi.+ Pa nthawi yomweyo, Asa anayamba kuponderezanso+ anthu ake ena. Miyambo 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu wosonyeza kukoma mtima kosatha amapindulitsa moyo wake,+ koma munthu wankhanza amachititsa kuti thupi lake linyanyalidwe.+
10 Koma Asa anamukwiyira wamasomphenyayo. Kenako anamuika m’ndende n’kumumanga m’matangadza+ popeza anamupsera mtima kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi.+ Pa nthawi yomweyo, Asa anayamba kuponderezanso+ anthu ake ena.
17 Munthu wosonyeza kukoma mtima kosatha amapindulitsa moyo wake,+ koma munthu wankhanza amachititsa kuti thupi lake linyanyalidwe.+