Genesis 42:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Nduna yaikulu ya dzikolo inalankhula nafe mwaukali,+ chifukwa inatiyesa akazitape okafufuza dzikolo.+ Miyambo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyankha modekha kumabweza mkwiyo,+ koma mawu opweteka amayambitsa mkwiyo.+ Miyambo 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu wosauka amalankhula mochonderera,+ koma munthu wolemera amayankha mwamphamvu.+ Mlaliki 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+
30 “Nduna yaikulu ya dzikolo inalankhula nafe mwaukali,+ chifukwa inatiyesa akazitape okafufuza dzikolo.+
12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+