2 Mbiri 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mfumuyo inayamba kuyankha anthuwo mwaukali.+ Chotero Mfumu Rehobowamu inasiya malangizo+ a akulu aja.+ Miyambo 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+
13 Mfumuyo inayamba kuyankha anthuwo mwaukali.+ Chotero Mfumu Rehobowamu inasiya malangizo+ a akulu aja.+
20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+