1 Mafumu 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano panali munthu+ wa Mulungu amene anatumidwa+ ndi Yehova kuchokera ku Yuda kupita ku Beteli. Kumeneko iye anapeza Yerobowamu ataimirira pambali pa guwa lansembe+ kuti afukize nsembe yautsi.+ 1 Mafumu 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mayiyo ataona zimenezi, anauza Eliya kuti: “Ndili nanu chiyani+ inu munthu wa Mulungu woona? Mwabwera kwa ine kudzandikumbutsa cholakwa changa+ ndi kudzapha mwana wanga.” Aheberi 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+
13 Tsopano panali munthu+ wa Mulungu amene anatumidwa+ ndi Yehova kuchokera ku Yuda kupita ku Beteli. Kumeneko iye anapeza Yerobowamu ataimirira pambali pa guwa lansembe+ kuti afukize nsembe yautsi.+
18 Mayiyo ataona zimenezi, anauza Eliya kuti: “Ndili nanu chiyani+ inu munthu wa Mulungu woona? Mwabwera kwa ine kudzandikumbutsa cholakwa changa+ ndi kudzapha mwana wanga.”
1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+