Genesis 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dzuwa linali litatuluka pamene Yakobo anali kuchoka pa Penueli, koma anali kuyenda chotsimphina.+ Oweruza 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero, anauzanso amuna a ku Penueli kuti: “Ndikabwerako bwino, ndidzagwetsa nsanja yanuyi.”+ Oweruza 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anagwetsanso+ nsanja ya ku Penueli+ ija, ndi kupha amuna a mumzindawo.