2 Mbiri 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Asa anamukwiyira wamasomphenyayo. Kenako anamuika m’ndende n’kumumanga m’matangadza+ popeza anamupsera mtima kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi.+ Pa nthawi yomweyo, Asa anayamba kuponderezanso+ anthu ake ena. Salimo 105:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+ Yeremiya 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya+ ndi kumuika m’matangadza+ amene anali pa Chipata Chakumtunda cha Benjamini, cha m’nyumba ya Yehova.
10 Koma Asa anamukwiyira wamasomphenyayo. Kenako anamuika m’ndende n’kumumanga m’matangadza+ popeza anamupsera mtima kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi.+ Pa nthawi yomweyo, Asa anayamba kuponderezanso+ anthu ake ena.
15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+
2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya+ ndi kumuika m’matangadza+ amene anali pa Chipata Chakumtunda cha Benjamini, cha m’nyumba ya Yehova.