Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 22:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma Balamu anayankha atumiki a Balaki aja kuti: “Ngakhale Balaki atandipatsa nyumba yake yodzaza siliva ndi golide, sindingachite chilichonse mosemphana ndi zimene Yehova Mulungu wanga angandilamule, kaya kuchotsera kapena kuwonjezerapo.+

  • Esitere 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako mfumu inamufunsa kuti: “Chavuta n’chiyani Mfumukazi Esitere, ndipo ukufuna kupempha chiyani?+ Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu,+ ipatsidwa kwa iwe.”

  • Esitere 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano mfumu inafunsanso Esitere pa tsiku lachiwiri la phwando la vinyo kuti:+ “Ukufuna kupempha chiyani+ Mfumukazi Esitere? Chimene ukufunacho ndikupatsa.+ Ukufuna chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu,+ ipatsidwa kwa iwe.”

  • Maliko 6:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndithu, anachita kumulumbirira kuti: “Chilichonse chimene ungapemphe kwa ine, ndidzachipereka kwa iwe,+ ngakhale hafu ya ufumu wangawu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena