1 Samueli 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero Sauli ndi mtumiki wake ananyamuka kupita kuphiri kuja, ndipo kumeneko anakumana ndi kagulu ka aneneri. Nthawi yomweyo, mzimu wa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa iye,+ moti anayamba kulankhula ngati mneneri+ pakati pa aneneriwo. Ezekieli 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, losera zokhudza aneneri a mu Isiraeli.+ Uuze amene akulosera zam’mutu mwawo+ kuti, ‘Mvetserani mawu a Yehova.+ Amosi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+
10 Chotero Sauli ndi mtumiki wake ananyamuka kupita kuphiri kuja, ndipo kumeneko anakumana ndi kagulu ka aneneri. Nthawi yomweyo, mzimu wa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa iye,+ moti anayamba kulankhula ngati mneneri+ pakati pa aneneriwo.
2 “Iwe mwana wa munthu, losera zokhudza aneneri a mu Isiraeli.+ Uuze amene akulosera zam’mutu mwawo+ kuti, ‘Mvetserani mawu a Yehova.+
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+