Miyambo 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nthongo imene wadya udzaisanza, ndipo mawu ako abwino adzakhala atapita pachabe.+