Numeri 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Yehova anamuika Balamu+ mawu m’kamwa, n’kumuuza kuti: “Bwerera kwa Balaki, ukamuuze mawu amenewa.”+ Numeri 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kumeneko Yehova analankhuladi ndi Balamu, n’kumuika mawu m’kamwa, ndipo anamuuza kuti:+ “Bwerera kwa Balaki+ ukamuuze zimenezi.” Numeri 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mawu a iye wakumva zonena za Mulungu,+Iye amene waona masomphenya a Wamphamvuyonse,+Pamene anali kugwa pansi, maso ake ali chipenyere.+ Mawu ake akuti:
5 Pamenepo Yehova anamuika Balamu+ mawu m’kamwa, n’kumuuza kuti: “Bwerera kwa Balaki, ukamuuze mawu amenewa.”+
16 Kumeneko Yehova analankhuladi ndi Balamu, n’kumuika mawu m’kamwa, ndipo anamuuza kuti:+ “Bwerera kwa Balaki+ ukamuuze zimenezi.”
4 Mawu a iye wakumva zonena za Mulungu,+Iye amene waona masomphenya a Wamphamvuyonse,+Pamene anali kugwa pansi, maso ake ali chipenyere.+ Mawu ake akuti: