1 Mafumu 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero, mneneri wokalambayo anakaika mtembowo m’manda ake. Ndipo anapitiriza kumulira+ kuti: “Kalanga ine, m’bale wanga!” 2 Mafumu 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho iye anati: “Musiyeni apume.+ Musalole aliyense kudodometsa mafupa ake.” Chotero iwo sanakhudze mafupa akewo limodzi ndi mafupa a mneneri+ amene anachokera ku Samariya.
30 Atatero, mneneri wokalambayo anakaika mtembowo m’manda ake. Ndipo anapitiriza kumulira+ kuti: “Kalanga ine, m’bale wanga!”
18 Choncho iye anati: “Musiyeni apume.+ Musalole aliyense kudodometsa mafupa ake.” Chotero iwo sanakhudze mafupa akewo limodzi ndi mafupa a mneneri+ amene anachokera ku Samariya.