Yobu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kwa Iye amene amakola anzeru m’kuchenjera kwawo,+Iye amene amachititsa kuti malangizo a ochenjera abweretse chisokonezo.+ Salimo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wasokoneza zolinga za anthu a mitundu ina.+Walepheretsa maganizo a mitundu ya anthu.+
13 Kwa Iye amene amakola anzeru m’kuchenjera kwawo,+Iye amene amachititsa kuti malangizo a ochenjera abweretse chisokonezo.+ Salimo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wasokoneza zolinga za anthu a mitundu ina.+Walepheretsa maganizo a mitundu ya anthu.+