1 Mafumu 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atatero, anamuuza Yerobowamu kuti: “Tengapo zidutswa 10, pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wati, ‘Ndikung’amba ufumuwu kuuchotsa m’manja mwa Solomo, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+ 1 Mafumu 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aisiraeli onse atangomva kuti Yerobowamu wabwera, nthawi yomweyo anatumiza uthenga womuitanira kumene anasonkhana, ndipo anamuika kukhala mfumu ya Aisiraeli onse.+ Palibenso amene ankatsatira nyumba ya Davide kupatula fuko la Yuda lokha.+ 1 Mafumu 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ngakhale kuti ndinakukweza kukuchotsa kufumbi+ kuti ukhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli,+ iwe wayenda m’njira ya Yerobowamu+ n’kuchimwitsa anthu anga Aisiraeli mwa kundikwiyitsa ndi machimo awo.+
31 Atatero, anamuuza Yerobowamu kuti: “Tengapo zidutswa 10, pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wati, ‘Ndikung’amba ufumuwu kuuchotsa m’manja mwa Solomo, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+
20 Aisiraeli onse atangomva kuti Yerobowamu wabwera, nthawi yomweyo anatumiza uthenga womuitanira kumene anasonkhana, ndipo anamuika kukhala mfumu ya Aisiraeli onse.+ Palibenso amene ankatsatira nyumba ya Davide kupatula fuko la Yuda lokha.+
2 “Ngakhale kuti ndinakukweza kukuchotsa kufumbi+ kuti ukhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli,+ iwe wayenda m’njira ya Yerobowamu+ n’kuchimwitsa anthu anga Aisiraeli mwa kundikwiyitsa ndi machimo awo.+