Deuteronomo 29:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Yehova anawazula m’dziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu n’kuwataya m’dziko lina monga mmene zilili lero.’+ 2 Mafumu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’chaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ n’kutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala+ ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani,+ ndiponso m’mizinda ya Amedi.+ Mateyu 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma iye anayankha kuti: “Mbewu iliyonse imene sinabzalidwe ndi Atate wanga wakumwamba idzazulidwa.+
28 Choncho Yehova anawazula m’dziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu n’kuwataya m’dziko lina monga mmene zilili lero.’+
6 M’chaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ n’kutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala+ ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani,+ ndiponso m’mizinda ya Amedi.+
13 Koma iye anayankha kuti: “Mbewu iliyonse imene sinabzalidwe ndi Atate wanga wakumwamba idzazulidwa.+