1 Mafumu 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero Solomo anayamba kufunafuna kupha Yerobowamu.+ Choncho Yerobowamu ananyamuka n’kuthawira+ ku Iguputo kwa Sisaki,+ mfumu ya Iguputo. Anakhala ku Iguputoko mpaka Solomo atamwalira. 2 Mbiri 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’chaka chachisanu cha Mfumu Rehobowamu,+ Sisaki+ mfumu ya Iguputo anabwera kudzaukira Yerusalemu (chifukwa iwo anachita zosakhulupirika kwa Yehova).+
40 Chotero Solomo anayamba kufunafuna kupha Yerobowamu.+ Choncho Yerobowamu ananyamuka n’kuthawira+ ku Iguputo kwa Sisaki,+ mfumu ya Iguputo. Anakhala ku Iguputoko mpaka Solomo atamwalira.
2 M’chaka chachisanu cha Mfumu Rehobowamu,+ Sisaki+ mfumu ya Iguputo anabwera kudzaukira Yerusalemu (chifukwa iwo anachita zosakhulupirika kwa Yehova).+