Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 14:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma iweyo unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iwe usanakhale. Unadzipangiranso mulungu wina+ ndi zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula+ kuti undikwiyitse,+ ndipo wandikankhira ineyo kumbuyo kwako.+

  • 1 Mafumu 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mawu a Yehova otsutsana ndi Basa ndi nyumba yake+ anafikira Yehu mwana wa Haneni mneneri. Mawuwo anali otsutsana naye chifukwa cha zoipa zonse zimene Basayo anachita pamaso pa Yehova mwa kumukwiyitsa+ ndi ntchito ya manja ake,+ ndiponso chifukwa chakuti iye anapha+ Nadabu. Mawuwo anali akuti nyumba yake idzakhala ngati nyumba ya Yerobowamu.

  • 1 Mafumu 16:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Omuri anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anachita zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iye asanakhale.+

  • 1 Mafumu 16:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ahabu mwana wa Omuri anachita zoipa kwambiri pamaso pa Yehova kuposa onse amene anakhalapo iye asanakhale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena