Genesis 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero Abulahamu anauza mtumiki wake yemwe anali wamkulu koposa m’nyumba yake, ndi woyang’anira zinthu zake zonse,+ kuti: “Chonde, ika dzanja lako pansi pa ntchafu yanga.+ Genesis 39:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Potifara anapitiriza kumukonda Yosefe pamene anali kum’tumikira, moti anamusankha kukhala woyang’anira nyumba yake.+ Zonse zimene Potifara anali nazo anazipereka m’manja mwa Yosefe.
2 Chotero Abulahamu anauza mtumiki wake yemwe anali wamkulu koposa m’nyumba yake, ndi woyang’anira zinthu zake zonse,+ kuti: “Chonde, ika dzanja lako pansi pa ntchafu yanga.+
4 Potifara anapitiriza kumukonda Yosefe pamene anali kum’tumikira, moti anamusankha kukhala woyang’anira nyumba yake.+ Zonse zimene Potifara anali nazo anazipereka m’manja mwa Yosefe.