Numeri 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Wobwezera magazi+ ndi amene ayenera kupha wakupha munthuyo. Akadzangom’peza, wobwezera magaziyo adzamuphe. Numeri 35:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndipo musalandire dipo lowombolera moyo wa munthu wakupha mnzake, chifukwa ndi woyenera kuphedwa.+ Aphedwe ndithu ameneyo.+
19 “‘Wobwezera magazi+ ndi amene ayenera kupha wakupha munthuyo. Akadzangom’peza, wobwezera magaziyo adzamuphe.
31 Ndipo musalandire dipo lowombolera moyo wa munthu wakupha mnzake, chifukwa ndi woyenera kuphedwa.+ Aphedwe ndithu ameneyo.+