Miyambo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu okhala m’dziko akamachimwa pamakhala akalonga ambiri otsatizanatsatizana,+ koma chifukwa cha munthu wozindikira, wodziwa zinthu zoyenera kuchita, kalonga amakhala kwa nthawi yaitali.+ Mateyu 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Podziwa maganizo awo,+ iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha,+ ndipo mzinda uliwonse kapena nyumba yogawanika siikhalitsa.
2 Anthu okhala m’dziko akamachimwa pamakhala akalonga ambiri otsatizanatsatizana,+ koma chifukwa cha munthu wozindikira, wodziwa zinthu zoyenera kuchita, kalonga amakhala kwa nthawi yaitali.+
25 Podziwa maganizo awo,+ iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha,+ ndipo mzinda uliwonse kapena nyumba yogawanika siikhalitsa.