Zefaniya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mzindawo sunafune kumvera,+ sunalole kulangizidwa,*+ sunakhulupirire Yehova+ ndipo sunayandikire Mulungu wake.+
2 Mzindawo sunafune kumvera,+ sunalole kulangizidwa,*+ sunakhulupirire Yehova+ ndipo sunayandikire Mulungu wake.+