2 Samueli 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano mu Isiraeli yense munalibe mwamuna wina wotamandika kwambiri koposa Abisalomu chifukwa cha kukongola kwake.+ Iye analibe chilema chilichonse kuyambira kuphazi mpaka paliwombo.
25 Tsopano mu Isiraeli yense munalibe mwamuna wina wotamandika kwambiri koposa Abisalomu chifukwa cha kukongola kwake.+ Iye analibe chilema chilichonse kuyambira kuphazi mpaka paliwombo.