Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 5:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 ‘Kodi sanapeze zofunkha ndipo ayenera kuzigawa?+

      Kodi sayenera kugawa mkazi mmodzi, kapenanso akazi awiri kwa mwamuna aliyense wamphamvu,+

      Ndi nsalu za Sisera zofunkhidwa zonyika mu utoto, ndithu nsalu zofunkhidwa zonyika mu utoto?

      Kodi sayenera kugawa chovala chopeta chonyika mu utoto, inde, zovala ziwiri zopeta,

      Kuti amuna ofunkha avale m’makosi awo?’

  • Ezara 8:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 mbale 20 zing’onozing’ono zagolide zolowa zokwana madariki* 1,000 ndi ziwiya ziwiri zamkuwa wabwino wonyezimira mofiirira, zamtengo wapatali ngati golide.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena