1 Mafumu 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya anasonkhanitsa gulu lake lonse lankhondo ndiponso mahatchi+ ndi magaleta.+ Atatero ananyamuka pamodzi ndi mafumu ena 32,+ n’kupita kukazungulira+ mzinda wa Samariya+ kuti amenyane nawo. 1 Mafumu 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo ananyamuka masana pamene Beni-hadadi anali kumwa ndi kuledzera+ m’misasa, pamodzi ndi mafumu ena 32 amene anali kumuthandiza aja.
20 Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya anasonkhanitsa gulu lake lonse lankhondo ndiponso mahatchi+ ndi magaleta.+ Atatero ananyamuka pamodzi ndi mafumu ena 32,+ n’kupita kukazungulira+ mzinda wa Samariya+ kuti amenyane nawo.
16 Iwo ananyamuka masana pamene Beni-hadadi anali kumwa ndi kuledzera+ m’misasa, pamodzi ndi mafumu ena 32 amene anali kumuthandiza aja.