Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iwo anali kubwera ndi ziweto zawo ndi mahema awo. Anali kubwera ochuluka kwambiri ngati dzombe,+ ndipo iwo ndi ngamila zawo anali osawerengeka.+ Iwo anali kubwera m’dzikomo n’kumaliwononga.+

  • 1 Samueli 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Afilisiti nawonso anasonkhana pamodzi kuti amenyane ndi Isiraeli. Iwo anali ndi magaleta ankhondo 30,000,*+ asilikali okwera pamahatchi 6,000 ndi anthu ochuluka kwambiri ngati mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Chotero anapita ku Mikimasi ndi kumanga misasa kum’mawa kwa Beti-aveni.+

  • 2 Mbiri 32:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.+ Musaope+ kapena kuchita mantha+ ndi mfumu ya Asuri+ ndi khamu lalikulu limene ili nalo,+ chifukwa ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi mfumuyo.

  • Aheberi 11:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Anagonjetsa mphamvu ya moto,+ anathawa lupanga,+ anali ofooka koma anapatsidwa mphamvu,+ analimba mtima pa nkhondo,+ ndiponso anagonjetsa magulu ankhondo a mayiko ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena