Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 34:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Tiyeni tidzisankhire chiweruzo.

      Tidziwe tokha pakati pathu chimene chili chabwino.

  • Luka 19:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iye anamuuza kuti, ‘Ndikuweruza mwa zotuluka pakamwa pako,+ kapolo woipa iwe. Ukuti unadziwa kuti ine ndine munthu wouma mtima, wotenga zimene sindinasungitse ndi kukolola zimene sindinafese?+

  • Agalatiya 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena