1 Mafumu 20:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu wina wochokera pakati pa ana a aneneri,*+ pomvera mawu+ a Yehova anauza mnzake kuti: “Ndimenye!” Koma mnzakeyo anakana kum’menya.
35 Munthu wina wochokera pakati pa ana a aneneri,*+ pomvera mawu+ a Yehova anauza mnzake kuti: “Ndimenye!” Koma mnzakeyo anakana kum’menya.