Numeri 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 mwa akulu a Isiraeli,+ amene ukuwadziwa kuti ndiwo akulu ndi oyang’anira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi nawe. Deuteronomo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama.
16 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 mwa akulu a Isiraeli,+ amene ukuwadziwa kuti ndiwo akulu ndi oyang’anira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi nawe.
18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama.