Yesaya 58:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndithu inuyo munali kusala kudya n’cholinga choti muzikangana, kulimbana,+ ndiponso kuti muzimenyana ndi nkhonya zovulaza.+ Kodi inuyo simunali kusala kudya n’kumaganiza kuti inali nthawi yoti mawu anu amveke kumwamba?
4 Ndithu inuyo munali kusala kudya n’cholinga choti muzikangana, kulimbana,+ ndiponso kuti muzimenyana ndi nkhonya zovulaza.+ Kodi inuyo simunali kusala kudya n’kumaganiza kuti inali nthawi yoti mawu anu amveke kumwamba?