1 Samueli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Antchito anu aamuna, antchito anu aakazi, abusa anu aluso kwambiri ndi abulu anu idzawatenganso kuti ikawagwiritse ntchito.+ 2 Mafumu 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yehu atamva mawu amenewa, anakweza maso kuyang’ana pawindopo, n’kufunsa kuti: “Ndani ali kumbali yanga? Ndani?”+ Nthawi yomweyo nduna ziwiri kapena zitatu za panyumba ya mfumu+ zinasuzumira pansi kuyang’ana Yehu.
16 Antchito anu aamuna, antchito anu aakazi, abusa anu aluso kwambiri ndi abulu anu idzawatenganso kuti ikawagwiritse ntchito.+
32 Yehu atamva mawu amenewa, anakweza maso kuyang’ana pawindopo, n’kufunsa kuti: “Ndani ali kumbali yanga? Ndani?”+ Nthawi yomweyo nduna ziwiri kapena zitatu za panyumba ya mfumu+ zinasuzumira pansi kuyang’ana Yehu.