Salimo 104:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mumapanga angelo anu kukhala mizimu,+Ndipo atumiki anu kukhala moto wonyeketsa.+ Aheberi 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amapanga angelo ake kukhala mizimu, ndipo amapanganso antchito ake otumikira ena kukhala lawi la moto.”+ Aheberi 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+
7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amapanga angelo ake kukhala mizimu, ndipo amapanganso antchito ake otumikira ena kukhala lawi la moto.”+
14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+