2 Mbiri 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo Mikaya anati: “Udzadziwa zimenezo tsiku+ limene udzalowe m’chipinda chamkati kukabisala.”+
24 Pamenepo Mikaya anati: “Udzadziwa zimenezo tsiku+ limene udzalowe m’chipinda chamkati kukabisala.”+