2 Mbiri 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamenepo Mikaya ananena kuti: “Mukakabwereradi mu mtendere, ndiye kuti Yehova sanalankhule nane.”+ Anatinso: “Imvani anthu nonsenu.”+
27 Pamenepo Mikaya ananena kuti: “Mukakabwereradi mu mtendere, ndiye kuti Yehova sanalankhule nane.”+ Anatinso: “Imvani anthu nonsenu.”+