Genesis 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mbiri ya Esau, kapena kuti Edomu,+ ili motere: Genesis 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano nayi mibadwo ya Esau, kholo la Aedomu, amene anali kukhala kudera lamapiri la Seiri.+