1 Mafumu 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ahabu mwana wa Omuri anachita zoipa kwambiri pamaso pa Yehova kuposa onse amene anakhalapo iye asanakhale.+ 2 Mafumu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anayenda m’njira ya anthu a m’nyumba ya Ahabu,+ ndipo anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova+ monga mmene anachitira a m’nyumba ya Ahabu, chifukwa anali wachibale wa nyumba ya Ahabu.+ 2 Mbiri 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ahaziya nayenso anayenda m’njira za anthu a m’nyumba ya Ahabu+ chifukwa amayi ake+ ndi amene anali kumulangiza kuti azichita zoipa.
30 Ahabu mwana wa Omuri anachita zoipa kwambiri pamaso pa Yehova kuposa onse amene anakhalapo iye asanakhale.+
27 Iye anayenda m’njira ya anthu a m’nyumba ya Ahabu,+ ndipo anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova+ monga mmene anachitira a m’nyumba ya Ahabu, chifukwa anali wachibale wa nyumba ya Ahabu.+
3 Ahaziya nayenso anayenda m’njira za anthu a m’nyumba ya Ahabu+ chifukwa amayi ake+ ndi amene anali kumulangiza kuti azichita zoipa.