Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mlandu umenewu ubwerere pamutu+ pa Yowabu ndi pa nyumba yonse ya bambo ake. M’nyumba ya Yowabu+ simudzasowa munthu wa nthenda yakukha kumaliseche+ ndiponso wakhate.+ Simudzasowanso mwamuna wogwira ndodo yowombera nsalu,+ wokanthidwa ndi lupanga kapena wosowa mkate!”+

  • Salimo 109:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Ana ake akhale amasiye,*+

      Ndipo mkazi wakenso akhale wamasiye.+

  • Mateyu 27:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Atanena izi anthu onse anayankha kuti: “Magazi ake akhala pa ife ndi pa ana athu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena