2 Samueli 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Davide atamva zimenezi pambuyo pake, ananena kuti: “Pamaso pa Yehova, ineyo ndi ufumu wanga, mlandu wa magazi+ a Abineri mwana wa Nera sukutikhudza mpaka kalekale.*
28 Davide atamva zimenezi pambuyo pake, ananena kuti: “Pamaso pa Yehova, ineyo ndi ufumu wanga, mlandu wa magazi+ a Abineri mwana wa Nera sukutikhudza mpaka kalekale.*