Levitiko 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Tsopano lamulo la nsembe yachiyanjano+ imene aliyense azipereka kwa Yehova lili motere: 2 Samueli 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Davide atamaliza kupereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano, anadalitsa+ anthu m’dzina la Yehova+ wa makamu. 1 Mbiri 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga m’chipululu ndi guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni.+
18 Davide atamaliza kupereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano, anadalitsa+ anthu m’dzina la Yehova+ wa makamu.
29 Koma pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga m’chipululu ndi guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni.+