Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 38:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yuda ataona mkaziyo, anaganiza kuti ndi hule+ chifukwa anali ataphimba nkhope yake.+

  • Deuteronomo 23:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Mwana wamkazi aliyense wachiisiraeli asakhale hule wa pakachisi,+ ndiponso mwana wamwamuna aliyense wachiisiraeli asakhale hule wa pakachisi.*+

  • Yoswa 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mzindawu wapatulidwa kuti uwonongedwe,+ pakuti mzindawu limodzi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova. Rahabi+ yekha, hule uja, musamuphe. Mum’siye ndi moyo, iye pamodzi ndi onse amene ali naye m’nyumba mwake, chifukwa iye anabisa azondi amene tinawatuma.+

  • Oweruza 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano Yefita+ wa ku Giliyadi+ anakhala mwamuna wamphamvu ndi wolimba mtima.+ Mayi ake anali hule,+ ndipo bambo ake omubereka anali Giliyadi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena