Deuteronomo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+ 2 Akorinto 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aka ndi kachitatu+ tsopano kukonza ulendo wobwera kwanuko. “Muzitsimikizira nkhani iliyonse mutamva umboni wa pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.”+
15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+
13 Aka ndi kachitatu+ tsopano kukonza ulendo wobwera kwanuko. “Muzitsimikizira nkhani iliyonse mutamva umboni wa pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.”+