2 Samueli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye ndi amene adzamangira dzina langa nyumba,+ ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+ 1 Mbiri 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye ndiye adzandimangire nyumba,+ ndipo ndithu ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+ 1 Mbiri 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iyeyo ndi amene adzamanga nyumba ya dzina langa.+ Adzakhala mwana+ wanga, ndipo ine ndidzakhala atate wake.+ Ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu+ pa Isiraeli ndipo sudzagwedezeka mpaka kalekale.’ 1 Mbiri 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kuwonjezera pamenepo, anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndiye adzamanga nyumba yanga+ ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndam’sankha kuti akhale mwana wanga+ ndipo ine ndidzakhala atate wake.+ Zekariya 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno udzamuuze kuti,“‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Munthu uyu+ dzina lake ndi Mphukira.+ Adzaphuka pamalo ake ndipo adzamanga kachisi wa Yehova.+
13 Iye ndi amene adzamangira dzina langa nyumba,+ ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+
12 Iye ndiye adzandimangire nyumba,+ ndipo ndithu ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+
10 Iyeyo ndi amene adzamanga nyumba ya dzina langa.+ Adzakhala mwana+ wanga, ndipo ine ndidzakhala atate wake.+ Ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu+ pa Isiraeli ndipo sudzagwedezeka mpaka kalekale.’
6 “Kuwonjezera pamenepo, anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndiye adzamanga nyumba yanga+ ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndam’sankha kuti akhale mwana wanga+ ndipo ine ndidzakhala atate wake.+
12 Ndiyeno udzamuuze kuti,“‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Munthu uyu+ dzina lake ndi Mphukira.+ Adzaphuka pamalo ake ndipo adzamanga kachisi wa Yehova.+