1 Mafumu 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chakudya cha kunyumba yachifumu ya Solomo tsiku lililonse chinkakhala ufa wosalala wokwana miyezo 30 ya kori,*+ ufa wamba wokwana miyezo 60 ya kori, 2 Mbiri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ineyo ndipereka chakudya cha antchito anu otola nkhuni ndi odula mitengo. Ndipereka tirigu wokwanira makori* 20,000,+ balere makori 20,000, vinyo mitsuko* 20,000,+ ndi mafuta mitsuko 20,000.”
22 Chakudya cha kunyumba yachifumu ya Solomo tsiku lililonse chinkakhala ufa wosalala wokwana miyezo 30 ya kori,*+ ufa wamba wokwana miyezo 60 ya kori,
10 Ineyo ndipereka chakudya cha antchito anu otola nkhuni ndi odula mitengo. Ndipereka tirigu wokwanira makori* 20,000,+ balere makori 20,000, vinyo mitsuko* 20,000,+ ndi mafuta mitsuko 20,000.”