Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni m’bale wako, kuti asamalowe konse m’malo oyera+ kuseri kwa nsalu yotchinga,+ patsogolo pa chivundikiro cha Likasa, kuopera kuti angafe,+ chifukwa ine ndidzaonekera mu mtambo+ pamwamba pa chivundikirocho.+

  • 2 Mbiri 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 ndi zoikapo nyale+ ndi nyale zake+ zagolide woyenga bwino, zoti aziziyatsa m’chipinda chamkati+ mogwirizana ndi lamulo.

  • 2 Mbiri 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako ansembe anabweretsa likasa la pangano la Yehova kumalo ake, kuchipinda chamkati+ cha nyumbayo, Malo Oyera Koposa,+ ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+

  • Aheberi 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena