1 Mafumu 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Natani+ anauza Bati-seba+ mayi wake wa Solomo+ kuti: “Kodi simunamve kuti Adoniya mwana wa Hagiti+ wakhala mfumu koma mbuye wathu Davide sakuzidziwa n’komwe zimenezi?
11 Kenako Natani+ anauza Bati-seba+ mayi wake wa Solomo+ kuti: “Kodi simunamve kuti Adoniya mwana wa Hagiti+ wakhala mfumu koma mbuye wathu Davide sakuzidziwa n’komwe zimenezi?