2 Mbiri 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ M’litali mwake chinali mikono 20+ mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Choncho m’lifupi mwake, chipindacho chinali mikono 20, ndipo anachikuta ndi golide wabwino wokwanira matalente* 600.
8 Kenako anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ M’litali mwake chinali mikono 20+ mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Choncho m’lifupi mwake, chipindacho chinali mikono 20, ndipo anachikuta ndi golide wabwino wokwanira matalente* 600.