2 Mafumu 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zipilala+ zamkuwa zimene zinali m’nyumba ya Yehova, zotengera zokhala ndi mawilo+ ndi chosungiramo madzi chamkuwa+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, Akasidi anaziphwanyaphwanya n’kutenga mkuwa wake kupita nawo ku Babulo.+ 2 Mbiri 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anapanga zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yozungulira+ imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo, ndiponso maukonde awiri+ okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pamwamba pa zipilalazo.
13 Zipilala+ zamkuwa zimene zinali m’nyumba ya Yehova, zotengera zokhala ndi mawilo+ ndi chosungiramo madzi chamkuwa+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, Akasidi anaziphwanyaphwanya n’kutenga mkuwa wake kupita nawo ku Babulo.+
12 Anapanga zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yozungulira+ imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo, ndiponso maukonde awiri+ okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pamwamba pa zipilalazo.