Ekisodo 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Upange beseni losambira lamkuwa ndi choikapo chake chamkuwa.+ Uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndipo uthiremo madzi.+ Ekisodo 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga beseni losambira lamkuwa+ ndi choikapo chake chamkuwa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito akalirole* a akazi otumikira, amene anali kutumikira mwadongosolo pachipata cha chihema chokumanako.+ 2 Mafumu 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zipilala+ zamkuwa zimene zinali m’nyumba ya Yehova, zotengera zokhala ndi mawilo+ ndi chosungiramo madzi chamkuwa+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, Akasidi anaziphwanyaphwanya n’kutenga mkuwa wake kupita nawo ku Babulo.+ Yeremiya 52:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zipilala zamkuwa+ zimene zinali panyumba ya Yehova, zotengera zokhala ndi mawilo+ ndi chosungiramo madzi chamkuwa+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, Akasidi anaziphwanyaphwanya n’kutenga mkuwa wakewo kupita nawo ku Babulo.+
18 “Upange beseni losambira lamkuwa ndi choikapo chake chamkuwa.+ Uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndipo uthiremo madzi.+
8 Kenako anapanga beseni losambira lamkuwa+ ndi choikapo chake chamkuwa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito akalirole* a akazi otumikira, amene anali kutumikira mwadongosolo pachipata cha chihema chokumanako.+
13 Zipilala+ zamkuwa zimene zinali m’nyumba ya Yehova, zotengera zokhala ndi mawilo+ ndi chosungiramo madzi chamkuwa+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, Akasidi anaziphwanyaphwanya n’kutenga mkuwa wake kupita nawo ku Babulo.+
17 Zipilala zamkuwa+ zimene zinali panyumba ya Yehova, zotengera zokhala ndi mawilo+ ndi chosungiramo madzi chamkuwa+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, Akasidi anaziphwanyaphwanya n’kutenga mkuwa wakewo kupita nawo ku Babulo.+