Ekisodo 25:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale, zikhale zagolide woyenga bwino.+ Numeri 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno azitenga nsalu yabuluu n’kuphimbira choikapo nyale,+ pamodzi ndi nyale zake,+ zopanira zake zozimitsira nyale,+ zoikamo phulusa la zingwe za nyale,+ ndi ziwiya zake zonse+ zosungiramo mafuta ogwiritsa ntchito nthawi zonse. 2 Mbiri 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anapanganso maluwa agolide, nyale zagolide, zopanira+ zagolide zozimitsira nyale, (golide wake anali woyengedwa bwino kwambiri,)
38 Zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale, zikhale zagolide woyenga bwino.+
9 Ndiyeno azitenga nsalu yabuluu n’kuphimbira choikapo nyale,+ pamodzi ndi nyale zake,+ zopanira zake zozimitsira nyale,+ zoikamo phulusa la zingwe za nyale,+ ndi ziwiya zake zonse+ zosungiramo mafuta ogwiritsa ntchito nthawi zonse.
21 Anapanganso maluwa agolide, nyale zagolide, zopanira+ zagolide zozimitsira nyale, (golide wake anali woyengedwa bwino kwambiri,)