1 Mafumu 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anaika akerubiwo m’chipinda chamkati, ndipo mapiko awo anali otambasula.+ Nsonga ya phiko la kerubi mmodzi inagunda khoma ndipo nsonga ya phiko la kerubi winayo inagundanso khoma lina. Mapiko awo anafika pakati pa nyumbayo, ndipo anagundana.+ Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+ Ezekieli 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Phokoso la mapiko a akerubiwo+ linali kumveka mpaka kubwalo lakunja. Phokosolo linali kumveka ngati kulankhula kwa Mulungu Wamphamvuyonse.+
27 Kenako anaika akerubiwo m’chipinda chamkati, ndipo mapiko awo anali otambasula.+ Nsonga ya phiko la kerubi mmodzi inagunda khoma ndipo nsonga ya phiko la kerubi winayo inagundanso khoma lina. Mapiko awo anafika pakati pa nyumbayo, ndipo anagundana.+
80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+
5 Phokoso la mapiko a akerubiwo+ linali kumveka mpaka kubwalo lakunja. Phokosolo linali kumveka ngati kulankhula kwa Mulungu Wamphamvuyonse.+