2 Samueli 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pita, ukauze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi iwe ungandimangire nyumba yoti ine ndikhalemo?+ 1 Mbiri 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye ndiye adzandimangire nyumba,+ ndipo ndithu ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+
5 “Pita, ukauze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi iwe ungandimangire nyumba yoti ine ndikhalemo?+
12 Iye ndiye adzandimangire nyumba,+ ndipo ndithu ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+